Miyambo 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mphatso yoperekedwa mwachinsinsi imathetsa mkwiyo,+Ndipo chiphuphu choperekedwa mwamseri* chimathetsa ukali waukulu.
14 Mphatso yoperekedwa mwachinsinsi imathetsa mkwiyo,+Ndipo chiphuphu choperekedwa mwamseri* chimathetsa ukali waukulu.