Miyambo 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Wolungama amasangalala akamachita chilungamo,+Koma anthu ochita zoipa amadana ndi chilungamo.