Miyambo 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nsembe ya munthu woipa ndi yonyansa.+ Ndiye kuli bwanji akaipereka ndi zolinga zoipa!*