Miyambo 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mboni yonena mabodza idzawonongedwa,+Koma munthu amene amamvetsera adzapereka umboni wa zinthu zimene anamva ndipo zidzamuyendera bwino.* Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:28 Nsanja ya Olonda,5/15/1987, tsa. 30
28 Mboni yonena mabodza idzawonongedwa,+Koma munthu amene amamvetsera adzapereka umboni wa zinthu zimene anamva ndipo zidzamuyendera bwino.*