Miyambo 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu woipa amadzionetsa ngati wolimba mtima,+Koma wolungama amasankha njira yoyenera kuyenda.+