Miyambo 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Minga ndi misampha zili mʼnjira ya munthu wochita zopotoka,Koma aliyense amene amaona kuti moyo wake ndi wamtengo wapatali, amakhala nazo kutali.+
5 Minga ndi misampha zili mʼnjira ya munthu wochita zopotoka,Koma aliyense amene amaona kuti moyo wake ndi wamtengo wapatali, amakhala nazo kutali.+