Miyambo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wofesa zosalungama adzakolola mavuto,+Ndipo ndodo ya ukali wake idzatha.+