Miyambo 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usamasunthe chizindikiro chakalekale cha malire,+Kapena kulowerera munda wa ana amasiye.