Miyambo 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana usalephere kumupatsa chilango.*+ Ngakhale utamukwapula ndi chikwapu, sangafe.