Miyambo 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa chidakwa komanso munthu wosusuka adzasauka,+Ndipo kuwodzera kudzaveka munthu nsanza.