Miyambo 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Usakopeke ndi kufiira kwa vinyo,Pamene akunyezimira mʼkapu nʼkumatsetserekera kukhosi mwamyaa!