Miyambo 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Udzakhala ngati munthu amene wagona pakatikati pa nyanja,Komanso ngati munthu amene wagona pansonga ya mtengo* wa ngalawa.
34 Udzakhala ngati munthu amene wagona pakatikati pa nyanja,Komanso ngati munthu amene wagona pansonga ya mtengo* wa ngalawa.