Miyambo 23:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Udzanena kuti: “Andimenya koma sindinamve kupweteka. Andikuntha koma sindinadziwe chilichonse. Kodi ndidzuka nthawi yanji?+ Ndikufuna ndikamwenso wina.” Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:35 Nsanja ya Olonda,1/1/2010, tsa. 6
35 Udzanena kuti: “Andimenya koma sindinamve kupweteka. Andikuntha koma sindinadziwe chilichonse. Kodi ndidzuka nthawi yanji?+ Ndikufuna ndikamwenso wina.”