Miyambo 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pulumutsa anthu amene atengedwa kuti akaphedwe,Ndipo amene akuyenda modzandira popita kukaphedwa uwathandize.+
11 Pulumutsa anthu amene atengedwa kuti akaphedwe,Ndipo amene akuyenda modzandira popita kukaphedwa uwathandize.+