Miyambo 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ukanena kuti: “Ifetu zimenezi sitimazidziwa,” Kodi amene amafufuza mitima sazindikira zimene zili mʼmaganizo mwako?+ Ndithudi, amene amakuyangʼanitsitsa adzadziwaNdipo adzabwezera munthu aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+
12 Ukanena kuti: “Ifetu zimenezi sitimazidziwa,” Kodi amene amafufuza mitima sazindikira zimene zili mʼmaganizo mwako?+ Ndithudi, amene amakuyangʼanitsitsa adzadziwaNdipo adzabwezera munthu aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+