Miyambo 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa aliyense woipa alibe tsogolo,+Ndipo nyale ya anthu oipa idzazimitsidwa.+