Miyambo 24:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndinaona kuti munali tchire lokhalokha.Zitsamba zoyabwa zinali paliponse mʼmundamo,Komanso mpanda wake wamiyala unali utagumuka.+
31 Ndinaona kuti munali tchire lokhalokha.Zitsamba zoyabwa zinali paliponse mʼmundamo,Komanso mpanda wake wamiyala unali utagumuka.+