Miyambo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa cha kuleza mtima munthu angathe kunyengerera munthu waudindo,Ndipo mawu okoma akhoza* kuthyola fupa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:15 Galamukani!,11/2010, tsa. 19 Nsanja ya Olonda,11/1/1986, tsa. 28
15 Chifukwa cha kuleza mtima munthu angathe kunyengerera munthu waudindo,Ndipo mawu okoma akhoza* kuthyola fupa.+