Miyambo 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ukapeza uchi udye umene ungakukwane,Chifukwa ukadya wambiri ungathe kuusanza.+