Miyambo 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Waulesi amanena kuti: “Mumsewu muli mkango wamphamvu,Mʼbwalo la mzinda mukuyendayenda mkango.”+