Miyambo 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu waulesi amapisa dzanja lake mʼmbale ya chakudya,Koma amalephera kulibweretsa pakamwa pake chifukwa chotopa kwambiri.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:15 Nsanja ya Olonda,4/15/1997, ptsa. 30-31
15 Munthu waulesi amapisa dzanja lake mʼmbale ya chakudya,Koma amalephera kulibweretsa pakamwa pake chifukwa chotopa kwambiri.+