Miyambo 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mawu a munthu wonenera ena zoipa ali ngati chakudya chokoma,*Akachimeza chimalowa mʼmimba.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:22 Nsanja ya Olonda,10/15/1989, tsa. 13