Miyambo 26:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mawu achikondi ochokera pakamwa pa munthu wa mtima woipa,+Ali ngati siliva wokutira phale. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:23 Nsanja ya Olonda,7/15/2003, tsa. 28