-
Miyambo 26:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Munthu amene amadana ndi ena amabisa chidanicho ndi milomo yake,
Koma mumtima mwake mumakhala chinyengo.
-
24 Munthu amene amadana ndi ena amabisa chidanicho ndi milomo yake,
Koma mumtima mwake mumakhala chinyengo.