Miyambo 26:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Amene akukumba dzenje adzagweramo yekha,Ndipo amene akugubuduza mwala udzabwerera kwa iye nʼkumupsinja.+
27 Amene akukumba dzenje adzagweramo yekha,Ndipo amene akugubuduza mwala udzabwerera kwa iye nʼkumupsinja.+