Miyambo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usadzitame ndi zimene udzachite mawaChifukwa sukudziwa zimene zidzachitike mawa.*+