Miyambo 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wochenjera akaona tsoka amabisala,+Koma wosadziwa zinthu amangopitabe ndipo amakumana ndi mavuto. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:12 Nsanja ya Olonda,7/1/2015, ptsa. 8-9
12 Munthu wochenjera akaona tsoka amabisala,+Koma wosadziwa zinthu amangopitabe ndipo amakumana ndi mavuto.