Miyambo 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Siliva amamuyengera mʼmbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera mungʼanjo,+Mofanana ndi zimenezi munthu amayesedwa ndi zimene anthu akunena pomutamanda.* Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:21 Nsanja ya Olonda,8/1/2011, tsa. 299/15/2006, tsa. 192/1/1998, tsa. 31
21 Siliva amamuyengera mʼmbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera mungʼanjo,+Mofanana ndi zimenezi munthu amayesedwa ndi zimene anthu akunena pomutamanda.*