-
Miyambo 27:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ngakhale utasinja chitsiru ndi musi
Ngati mmene umasinjira mbewu mumtondo,
Uchitsiru wake sungachichokere.
-
22 Ngakhale utasinja chitsiru ndi musi
Ngati mmene umasinjira mbewu mumtondo,
Uchitsiru wake sungachichokere.