Miyambo 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu amene amachulukitsa chuma chake polandira chiwongoladzanja+ ndi katapira,Chuma chakecho chidzapita kwa munthu amene amakomera mtima anthu osauka.+
8 Munthu amene amachulukitsa chuma chake polandira chiwongoladzanja+ ndi katapira,Chuma chakecho chidzapita kwa munthu amene amakomera mtima anthu osauka.+