Miyambo 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu amene amasocheretsa anthu owongoka mtima kuti azichita zinthu zoipa, adzagwera mʼdzenje lake lomwe,+Koma anthu osalakwa adzalandira zinthu zabwino.+
10 Munthu amene amasocheretsa anthu owongoka mtima kuti azichita zinthu zoipa, adzagwera mʼdzenje lake lomwe,+Koma anthu osalakwa adzalandira zinthu zabwino.+