Miyambo 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Wosangalala ndi munthu amene nthawi zonse amasamala zochita zake,*Koma amene amaumitsa mtima wake adzakumana ndi tsoka.+
14 Wosangalala ndi munthu amene nthawi zonse amasamala zochita zake,*Koma amene amaumitsa mtima wake adzakumana ndi tsoka.+