Miyambo 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amene amayenda mosalakwitsa kanthu adzapulumutsidwa,+Koma amene njira zake ndi zokhotakhota adzagwa mwadzidzidzi.+
18 Amene amayenda mosalakwitsa kanthu adzapulumutsidwa,+Koma amene njira zake ndi zokhotakhota adzagwa mwadzidzidzi.+