Miyambo 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Aliyense amene amadalira mtima wake ndi wopusa,+Koma amene amachita zinthu mwanzeru adzapulumuka.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:26 Nsanja ya Olonda,11/1/2005, tsa. 22
26 Aliyense amene amadalira mtima wake ndi wopusa,+Koma amene amachita zinthu mwanzeru adzapulumuka.+