Miyambo 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Aliyense amene amapereka zinthu zake kwa anthu osauka sadzasowa kanthu,+Koma amene amatseka maso ake kuti asaone osaukawo adzalandira matemberero ambiri.
27 Aliyense amene amapereka zinthu zake kwa anthu osauka sadzasowa kanthu,+Koma amene amatseka maso ake kuti asaone osaukawo adzalandira matemberero ambiri.