Miyambo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu amene amaumitsa khosi lake* pambuyo podzudzulidwa mobwerezabwereza+Adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo sadzachira.+
29 Munthu amene amaumitsa khosi lake* pambuyo podzudzulidwa mobwerezabwereza+Adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo sadzachira.+