Miyambo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumu ikamachita zinthu zachilungamo dziko limalimba,+Koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.