Miyambo 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Oipa akachuluka, machimo amachuluka,Koma olungama adzaona oipawo akugwa.+