Miyambo 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Langa mwana wako ndipo adzakupatsa mpumuloKomanso adzakusangalatsa kwambiri.+