Miyambo 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Wantchito safuna kusintha ndi mawu okha,Chifukwa ngakhale atamvetsa mawuwo, safuna kuwatsatira.+