Miyambo 29:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Amene amathandiza munthu wakuba amadzibweretsera mavuto. Iye angamve kuitana kuti akapereke umboni,* koma osakanena chilichonse.+
24 Amene amathandiza munthu wakuba amadzibweretsera mavuto. Iye angamve kuitana kuti akapereke umboni,* koma osakanena chilichonse.+