Miyambo 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usawonjezere kanthu pa mawu ake+Kuti angakudzudzule,Nʼkuoneka kuti ndiwe wabodza.