Miyambo 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usanenere wantchito zoipa kwa bwana wake,Kuti angakutemberere ndipo ungapezeke wolakwa.+