-
Miyambo 30:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Njira ya chiwombankhanga mumlengalenga,
Njira ya njoka pamwala,
Njira ya sitima pakatikati pa nyanja,
Ndiponso njira ya mwamuna ndi mtsikana.
-