Miyambo 30:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Chifukwa mkaka ukaukhutchumula umatulutsa mafuta,Mphuno ukaifinya imatulutsa magazi,Ndipo kukolezera mkwiyo kumayambitsa mkangano.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:33 Nsanja ya Olonda,2/1/2008, tsa. 195/15/1987, tsa. 30
33 Chifukwa mkaka ukaukhutchumula umatulutsa mafuta,Mphuno ukaifinya imatulutsa magazi,Ndipo kukolezera mkwiyo kumayambitsa mkangano.+