-
Mlaliki 1:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Mphepo imapita kumʼmwera ndipo imazungulira mpaka kukafika kumpoto.
Imangozungulira mobwerezabwereza. Mphepoyo imapitiriza kuzungulira.
-