Mlaliki 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Palibe amene amakumbukira anthu akale.Ndipo palibe amene adzakumbukire amene anabwera pambuyo pa anthu akalewo.Iwowanso sadzakumbukiridwa ndi amene adzabwere pambuyo pawo.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:11 Nsanja ya Olonda,2/15/1997, tsa. 9
11 Palibe amene amakumbukira anthu akale.Ndipo palibe amene adzakumbukire amene anabwera pambuyo pa anthu akalewo.Iwowanso sadzakumbukiridwa ndi amene adzabwere pambuyo pawo.+