Mlaliki 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ndinanena mumtima mwanga kuti: “Ine ndapeza nzeru zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu+ ine ndisanakhalepo. Ndipo mtima wanga wamvetsa zinthu zambiri chifukwa cha nzeru ndi kudziwa zinthu.”+
16 Choncho ndinanena mumtima mwanga kuti: “Ine ndapeza nzeru zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu+ ine ndisanakhalepo. Ndipo mtima wanga wamvetsa zinthu zambiri chifukwa cha nzeru ndi kudziwa zinthu.”+