Mlaliki 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndinapeza siliva ndi golide wambiri,+ chuma chimene mafumu amakhala nacho* ndiponso chimene chimapezeka mʼzigawo za dziko.+ Ndinali ndi oimba aamuna ndi aakazi. Ndinalinso ndi akazi ambiri, omwe amasangalatsa kwambiri mtima wa amuna. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Nsanja ya Olonda,3/15/2011, tsa. 7
8 Ndinapeza siliva ndi golide wambiri,+ chuma chimene mafumu amakhala nacho* ndiponso chimene chimapezeka mʼzigawo za dziko.+ Ndinali ndi oimba aamuna ndi aakazi. Ndinalinso ndi akazi ambiri, omwe amasangalatsa kwambiri mtima wa amuna.