Mlaliki 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako ndinayamba kuganizaganiza kuti nzeru nʼchiyani, misala nʼchiyani ndiponso kuti uchitsiru nʼchiyani.+ (Kodi munthu amene wabwera pambuyo pa mfumu angachite chiyani? Zimene angachite nʼzimene anthu ena anachita kale.)
12 Kenako ndinayamba kuganizaganiza kuti nzeru nʼchiyani, misala nʼchiyani ndiponso kuti uchitsiru nʼchiyani.+ (Kodi munthu amene wabwera pambuyo pa mfumu angachite chiyani? Zimene angachite nʼzimene anthu ena anachita kale.)